Ezekieli 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anandipititsa kubwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyeramo+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka miyala. Pabwalo lowaka miyalalo panali zipinda zodyeramo zokwana 30.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 149/15/1988, ptsa. 26-27
17 Kenako anandipititsa kubwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyeramo+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka miyala. Pabwalo lowaka miyalalo panali zipinda zodyeramo zokwana 30.+