-
1 Mafumu 8:64Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
64 Tsiku limenelo, pakati pa bwalo la nyumba ya Yehova+ panayenera kupatulidwa ndi mfumu, chifukwa inafunika kuperekerapo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta a nsembe zachiyanjano. Inatero popeza guwa lansembe lamkuwa+ limene lili pamaso pa Yehova linachepa, ndipo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta+ a nsembe zachiyanjano sizikanakwanapo.
-