Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 38:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anapanganso nyanga+ m’makona ake anayi. Nyanga zakezo zinatuluka m’makona akewo, ndipo guwalo analikuta ndi mkuwa.+

  • Numeri 16:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 zofukizira za amuna amene anafa+ chifukwa cha kuchimwa. Azisule kuti zikhale timalata topyapyala n’kukutira nato guwa lansembe,+ popeza anafika nazo pamaso pa Yehova, ndipo zakhala zopatulika. Timalatato tikhale chikumbutso kwa ana a Isiraeli.’”+

  • 2 Mbiri 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lamkuwa.+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena