22 Tsopano Solomo anaimirira kutsogolo kwa guwa lansembe+ la Yehova pamaso pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+
14 Tsopano guwa lansembe+ lamkuwa limene linali pamaso pa Yehova, Ahazi analichotsa kutsogolo kwa nyumbayo. Analichotsa pakati pa guwa lansembe latsopano ndi nyumba ya Yehova,+ n’kuliika kumpoto kwa guwa lake.