2 Mbiri 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo guwa lansembe lamkuwa+ limene Bezaleli+ mwana wa Uri mwana wa Hura+ anapanga, anali ataliika patsogolo pa chihema chopatulika cha Yehova. Choncho Solomo ndi mpingowo anafunsira paguwalo monga mwa nthawi zonse.
5 Ndipo guwa lansembe lamkuwa+ limene Bezaleli+ mwana wa Uri mwana wa Hura+ anapanga, anali ataliika patsogolo pa chihema chopatulika cha Yehova. Choncho Solomo ndi mpingowo anafunsira paguwalo monga mwa nthawi zonse.