Ekisodo 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova.+ Mabingu ndi matalala asiya, kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+ Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+ Salimo 63:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho ndidzakutamandani pa nthawi yonse ya moyo wanga.+Ndidzapemphera m’dzina lanu nditakweza manja anga.+
29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova.+ Mabingu ndi matalala asiya, kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+
4 Choncho ndidzakutamandani pa nthawi yonse ya moyo wanga.+Ndidzapemphera m’dzina lanu nditakweza manja anga.+