1 Mafumu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu Solomo itatero, inalumbira pamaso pa Yehova kuti: “Mulungu andilange mowirikiza+ ngati Adoniya sanaike moyo wake pangozi mwa kupempha zimenezi.+ Miyambo 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 koma wolephera kundipeza akupweteka moyo wake.+ Onse odana ndi ine ndiye kuti amakonda imfa.”+
23 Mfumu Solomo itatero, inalumbira pamaso pa Yehova kuti: “Mulungu andilange mowirikiza+ ngati Adoniya sanaike moyo wake pangozi mwa kupempha zimenezi.+