Ekisodo 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo la chihema chopatulika.+ Kumbali ya ku Negebu, chakum’mwera, bwalolo analitchinga ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mikono 100 kutalika kwake kumbali imodziyo.+
9 Ndiyeno anapanga bwalo la chihema chopatulika.+ Kumbali ya ku Negebu, chakum’mwera, bwalolo analitchinga ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mikono 100 kutalika kwake kumbali imodziyo.+