Ekisodo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Ndiyeno upange bwalo+ la chihema chopatulika. Kumbali ya ku Negebu, chakum’mwera, bwalolo ulitchinge ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Mpandawo ukhale mikono 100 m’litali mwake kumbali imodziyo.
9 “Ndiyeno upange bwalo+ la chihema chopatulika. Kumbali ya ku Negebu, chakum’mwera, bwalolo ulitchinge ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Mpandawo ukhale mikono 100 m’litali mwake kumbali imodziyo.