Ekisodo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako udzatchinge bwalo+ la chihema chopatulika ndi mpanda, ndipo pachipata cha bwalolo udzakolowekepo nsalu yake yotchinga.+ Salimo 84:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+ Salimo 92:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu obzalidwa m’nyumba ya Yehova,+M’mabwalo a Mulungu wathu,+ adzakula mosangalala.
8 Kenako udzatchinge bwalo+ la chihema chopatulika ndi mpanda, ndipo pachipata cha bwalolo udzakolowekepo nsalu yake yotchinga.+
2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+