1 Mafumu 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza. Yohane 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo Yesu anali kuyenda m’kachisimo, m’khonde la zipilala la Solomo.+ Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+
36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.
12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+