Yohane 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo Yesu anali kuyenda m’kachisimo, m’khonde la zipilala la Solomo.+ Machitidwe 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munthu uja atakangamira Petulo ndi Yohane osawasiya, anthu onse pamodzi anakhamukira kwa iwo pamalo otchedwa khonde la zipilala la Solomo,+ ali odabwa kwambiri.
11 Tsopano munthu uja atakangamira Petulo ndi Yohane osawasiya, anthu onse pamodzi anakhamukira kwa iwo pamalo otchedwa khonde la zipilala la Solomo,+ ali odabwa kwambiri.