Machitidwe 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munthu uja atakangamira Petulo ndi Yohane osawasiya, anthu onse pamodzi anakhamukira kwa iwo pamalo otchedwa khonde la zipilala la Solomo,+ ali odabwa kwambiri. Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+
11 Tsopano munthu uja atakangamira Petulo ndi Yohane osawasiya, anthu onse pamodzi anakhamukira kwa iwo pamalo otchedwa khonde la zipilala la Solomo,+ ali odabwa kwambiri.
12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+