Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mfumu ya Babulo inatenga chuma chonse cha m’nyumba ya Yehova ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Inaphwanyaphwanyanso ziwiya zonse+ zagolide zimene Solomo mfumu ya Isiraeli anapangira kachisi wa Yehova, monga momwe Yehova ananenera.

  • 2 Mbiri 36:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mfumuyo inatenga ziwiya zonse,+ zazikulu+ ndi zazing’ono, za m’nyumba ya Mulungu woona. Inatenganso chuma+ cha m’nyumba ya Yehova, chuma cha mfumu+ ndi cha akalonga ake. Inatenga chilichonse n’kupita nacho ku Babulo.

  • Salimo 74:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iwo atentha malo anu opatulika.+

      Aipitsa ndi kugwetsera pansi chihema chokhala ndi dzina lanu.+

  • Maliro 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.

      Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+

      Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena