Ekisodo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa. Salimo 74:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitani kumalo amene awonongedwa.+M’malo oyera, mdani wachitira zoipa china chilichonse.+
17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.