Danieli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero la mtumiki wanu ndi kuchonderera kwake. Malo anu opatulika amene awonongedwa+ akomereni mtima,+ inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu. Mika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Yehova akuchoka pamalo ake,+ ndipo atsika ndi kupondaponda m’malo okwezeka a padziko lapansi.+
17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero la mtumiki wanu ndi kuchonderera kwake. Malo anu opatulika amene awonongedwa+ akomereni mtima,+ inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu.
3 Tamverani! Yehova akuchoka pamalo ake,+ ndipo atsika ndi kupondaponda m’malo okwezeka a padziko lapansi.+