Yesaya 64:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mizinda yanu yoyera+ yasanduka chipululu. Ziyoni+ wangosanduka chipululu basi, ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+ Maliro 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhandwe zayamba kuyendayenda paphiri la Ziyoni chifukwa lasanduka bwinja.+
10 Mizinda yanu yoyera+ yasanduka chipululu. Ziyoni+ wangosanduka chipululu basi, ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+