Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.