Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+ Yeremiya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+
26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+
2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+