Maliro 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+
9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+