Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Masiku ambiri Aisiraeli+ anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa+ ndiponso opanda Chilamulo.

  • Ezekieli 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 M’dzikolo mudzakhala mavuto otsatizanatsatizana+ ndipo muzidzamveka mauthenga otsatizanatsatizana. Anthu azidzafunafuna masomphenya kwa mneneri.+ Ansembe sadzathanso kuphunzitsa malamulo aphindu. Anthu achikulire sadzaperekanso malangizo othandiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena