Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+

      Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+

      Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+

      Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+

  • 2 Mbiri 17:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu.

  • Nehemiya 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Nehemiya+ amene ndiye Tirisata+ komanso Ezara+ wansembe, wokopera Malemba, ndi Alevi amene anali kupereka malangizo kwa anthu, anauza anthuwo kuti: “Lero ndi tsiku lopatulika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musakhale achisoni ndipo musalire.”+ Ananena zimenezi chifukwa anthu onse anali kulira pamene anali kumvetsera mawu a m’chilamulo.+

  • Malaki 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena