Levitiko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.” Deuteronomo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+ 2 Mbiri 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Masiku ambiri Aisiraeli+ anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa+ ndiponso opanda Chilamulo. Nehemiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+
11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.”
8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+
3 Masiku ambiri Aisiraeli+ anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa+ ndiponso opanda Chilamulo.
8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+