Hagai 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hagai mthenga+ wa Yehova analankhula kwa anthuwo malinga ndi ntchito imene Yehova anam’patsa.+ Iye anati: “‘Ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova.”
13 Hagai mthenga+ wa Yehova analankhula kwa anthuwo malinga ndi ntchito imene Yehova anam’patsa.+ Iye anati: “‘Ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova.”