Levitiko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.” Nehemiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+
11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.”
7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+