Nehemiya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yesuwa, Bani, Kadimiyeli, Sebaniya,+ Buni, Serebiya, Bani ndi Kenani anakwera pansanja+ ya Alevi ndi kuyamba kufuula kwa Yehova Mulungu wawo ndi mawu amphamvu.+
4 Ndiyeno Yesuwa, Bani, Kadimiyeli, Sebaniya,+ Buni, Serebiya, Bani ndi Kenani anakwera pansanja+ ya Alevi ndi kuyamba kufuula kwa Yehova Mulungu wawo ndi mawu amphamvu.+