2 Mbiri 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Alevi+ omwe anali ana a Kohati+ ndi ana a Kora+ anaimirira ndi kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+ Salimo 77:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Ndidzafuulira Mulungu,+Ndithu, ndidzafuulira Mulungu, ndipo iye adzatchera khutu lake kwa ine.+
19 Kenako Alevi+ omwe anali ana a Kohati+ ndi ana a Kora+ anaimirira ndi kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+