Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+ Salimo 116:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti watchera khutu lake kwa ine,+Ndipo ndidzaitanira pa iye masiku onse a moyo wanga.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+