Salimo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzafuulira Yehova mokweza,Ndipo iye adzandiyankha m’phiri lake loyera.+ [Seʹlah.] Salimo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+
17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+