1 Mbiri 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli makolo athu,+ thandizani anthu awa kuti apitirizebe kukhala ndi mtima wodzipereka woterewu,+ ndiponso kuti akutumikireni ndi mtima wawo wonse.+ 2 Mbiri 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dzanja la Mulungu woona linakhalanso ndi anthu a ku Yuda, moti anawapatsa mtima umodzi+ kuti amvere lamulo+ la mfumu ndi la akalonga pa nkhani zokhudza kutumikira Yehova.+
18 Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli makolo athu,+ thandizani anthu awa kuti apitirizebe kukhala ndi mtima wodzipereka woterewu,+ ndiponso kuti akutumikireni ndi mtima wawo wonse.+
12 Dzanja la Mulungu woona linakhalanso ndi anthu a ku Yuda, moti anawapatsa mtima umodzi+ kuti amvere lamulo+ la mfumu ndi la akalonga pa nkhani zokhudza kutumikira Yehova.+