Deuteronomo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu. Mlaliki 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikunena kuti: “Sunga lamulo la mfumu.+ Chita zimenezi polemekeza lumbiro la Mulungu.+ 1 Atesalonika 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti mukudziwa malamulo+ amene tinakupatsani mwa ulamuliro wa Ambuye Yesu.
5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.