Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+

  • 1 Mafumu 8:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mumve pemphero lopempha chifundo+ la mtumiki wanu ndi la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayang’ana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+

  • 1 Mafumu 8:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 inuyo mumve muli kumwamba pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo, ndipo muonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa iwo.+

  • Salimo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndipo adzanena kuti: “Inetu ndakhazika mfumu yanga+

      Pa Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”+

  • Yesaya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo. Iye akatiphunzitsa njira zake, ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena