Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ‘Likatigwera tsoka,+ lupanga, chiweruzo chowawa, mliri+ kapena njala,+ tiziima pamaso pa nyumba iyi+ ndi pamaso panu (popeza dzina lanu+ lili m’nyumba iyi), kuti tifuulire inu kuti mutithandize m’masautso athu, ndipo inu muzimva ndi kutipulumutsa.’+

  • Nehemiya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chonde, tsegulani maso anu ndi kutchera khutu+ kuti mumve pemphero la ine mtumiki wanu+ limene ndikupemphera pamaso panu lero. Usana ndi usiku+ ndikupempherera atumiki anu, ana a Isiraeli. Pochita zimenezi ndikuvomereza+ machimo+ a ana a Isiraeli amene tinakuchimwirani. Tonse tinachimwa, ine pamodzi ndi nyumba ya bambo anga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena