2 Mbiri 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano. 2 Mbiri 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano maso anga+ akhala otseguka ndipo makutu anga+ azimvetsera mapemphero onenedwa pamalo ano.
40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano.