Salimo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+ Salimo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+
17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+
2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+