Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano maso anga+ akhala otseguka ndipo makutu anga+ azimvetsera mapemphero onenedwa pamalo ano.

  • 2 Mbiri 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+

  • Salimo 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+

      Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+

      Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.

  • Salimo 34:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+

      Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+

  • Yesaya 37:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu onse a Senakeribu+ amene watumiza kudzatonza nawo Mulungu wamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena