2 Mbiri 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano. Salimo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ Salimo 71:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+ Salimo 130:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga Yehova.+Makutu anu amve mawu anga ochonderera.+
40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano.
6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+
2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+