Salimo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa. Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+
4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa.