Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+ Yesaya 45:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 kuti, ‘Zoonadi, kwa Yehova kuli chilungamo chonse ndi mphamvu.+ Onse omukwiyira adzabwereranso kwa iyeyo n’kuchita manyazi.+ Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+
7 Pakuti Yehova ndi wolungama.+ Amakonda ntchito zolungama.+Anthu owongoka mtima ndi amene adzaona nkhope yake.+
24 kuti, ‘Zoonadi, kwa Yehova kuli chilungamo chonse ndi mphamvu.+ Onse omukwiyira adzabwereranso kwa iyeyo n’kuchita manyazi.+
6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+