Salimo 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+ Salimo 146:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+
7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+
8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+