2 Mbiri 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano. Salimo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+ Salimo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+
40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano.
17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+
6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+