Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+ Salimo 79:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezerani anthu oyandikana nafe mwa kuwatsanulira chitonzo pachifuwa pawo maulendo 7,+Inu Yehova, muwabwezere chitonzo chimene anachita pa inu.+ Yesaya 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwina Yehova Mulungu amva mawu onse a Rabisake,+ amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira amene alipo.’”+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+
12 Bwezerani anthu oyandikana nafe mwa kuwatsanulira chitonzo pachifuwa pawo maulendo 7,+Inu Yehova, muwabwezere chitonzo chimene anachita pa inu.+
4 Mwina Yehova Mulungu amva mawu onse a Rabisake,+ amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira amene alipo.’”+