Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova atamva zimenezi anauza Kaini kuti: “Pa chifukwa chimenechi, aliyense amene adzaphe Kaini adzalangidwa maulendo 7.”+

      Choncho Yehova anaikira Kaini chizindikiro kuti aliyense womupeza asamuphe.+

  • Yesaya 65:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Taonani! Zalembedwa pamaso panga.+ Ine sindidzakhala chete,+ koma ndidzapereka mphoto.+ Mphotoyo ndidzaiika pachifuwa pawo,+

  • Yeremiya 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo + amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula pamalo awo.+ Ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.+

  • Yeremiya 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+

  • Luka 6:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Khalani opatsa ndipo inunso anthu adzakupatsani.+ Adzakhuthulira m’matumba anu muyezo wabwino, wotsendereka, wokhutchumuka ndi wosefukira. Pakuti muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena