Genesis 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati wopha Kaini ati adzalangidwe maulendo 7,+Ndiyetu wopha ine Lameki, adzalangidwa maulendo 77.” Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ Aheberi 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+
24 Ngati wopha Kaini ati adzalangidwe maulendo 7,+Ndiyetu wopha ine Lameki, adzalangidwa maulendo 77.”
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+