Genesis 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova atamva zimenezi anauza Kaini kuti: “Pa chifukwa chimenechi, aliyense amene adzaphe Kaini adzalangidwa maulendo 7.”+ Choncho Yehova anaikira Kaini chizindikiro kuti aliyense womupeza asamuphe.+ Levitiko 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.
15 Yehova atamva zimenezi anauza Kaini kuti: “Pa chifukwa chimenechi, aliyense amene adzaphe Kaini adzalangidwa maulendo 7.”+ Choncho Yehova anaikira Kaini chizindikiro kuti aliyense womupeza asamuphe.+
18 “‘Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu amtundu wako.+ Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.