Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 “Inu munamva kuti anati, ‘Uzikonda mnzako+ ndi kudana ndi mdani wako.’+

  • Mateyu 22:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Lachiwiri lofanana nalo ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+

  • Aroma 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chifukwa malamulo onena kuti, “Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,+ Usabe,+ Usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili m’mawu awa akuti, “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+

  • Agalatiya 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Chilamulo chonse chimakwaniritsidwa+ m’mawu akuti: “Uzikonda mnzako ngati mmene umadzikondera wekha.”+

  • Yakobo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena