Ekisodo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ukapeza ng’ombe kapena bulu wa mdani wako atasochera, um’bweze ndithu kwa mwiniwake.+