Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Usachite chigololo.+

  • Malaki 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Anthu inu ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni.+ Sindidzazengereza kupereka umboni+ wotsutsa amatsenga,+ achigololo,+ olumbira monama+ komanso ochita chinyengo pa malipiro a munthu waganyu.+ Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa anthu ochitira chinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye*+ ndiponso opondereza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Mateyu 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+

  • Mateyu 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma iye anafunsa Yesu kuti: “Malamulo ati?”+ Yesu anati: “Akuti, Usaphe+ munthu,* Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonamizira mnzako.+

  • 1 Akorinto 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena