Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+ Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.