Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?